Yohane 12:14 - Buku Lopatulika14 Koma Yesu, m'mene adapeza kabulu anakhala pamenepo; monga mulembedwa: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Koma Yesu, m'mene adapeza kabulu anakhala pamenepo; monga mulembedwa: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono Yesu adapeza mwanawabulu nakwerapo, monga akunenera Malembo kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Yesu anapeza bulu wamngʼono ndi kukwerapo, monga kunalembedwa kuti: Onani mutuwo |