Yohane 12:10 - Buku Lopatulika10 Koma ansembe aakulu anapangana kuti akaphe Lazaronso; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma ansembe aakulu anapangana kuti akaphe Lazaronso; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Motero akulu a ansembe adaapangana zoti aphe ndi Lazaro yemwe, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Choncho akulu a ansembe anakonza njira yoti aphenso Lazaro, Onani mutuwo |