Yohane 11:43 - Buku Lopatulika43 Ndipo m'mene adanena izi, anafuula ndi mau aakulu, Lazaro, tuluka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndipo m'mene adanena izi, anafuula ndi mau akulu, Lazaro, tuluka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Atatero adaitana mokweza mau kuti, “Lazaro, tuluka!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Yesu atanena izi, Iye anayitana ndi mawu ofuwula kuti, “Lazaro, tuluka!” Onani mutuwo |