Yohane 11:23 - Buku Lopatulika23 Yesu ananena naye, Mlongo wako adzauka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Yesu ananena naye, Mlongo wako adzauka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Yesu adamuuza kuti, “Mlongo wako adzauka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Yesu anati kwa iye, “Mlongo wako adzauka.” Onani mutuwo |