Yohane 11:1 - Buku Lopatulika1 Koma panali munthu wodwala, Lazaro wa ku Betaniya, wa m'mudzi wa Maria ndi mbale wake Marita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma panali munthu wodwala, Lazaro wa ku Betaniya, wa m'mudzi wa Maria ndi mbale wake Marita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Panali munthu wina, dzina lake Lazaro, amene ankadwala. Anali wa ku mudzi wa Betaniya, kwao kwa Maria ndi mbale wake Marita. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsopano munthu wina dzina lake Lazaro anadwala. Iye anali wa ku Betaniya, mudzi wa Mariya ndi mchemwali wake Marita. Onani mutuwo |