Yohane 10:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo anachoka kunkanso tsidya lija la Yordani, kumalo kumene kunali Yohane analikubatiza poyamba paja; ndipo anakhala komweko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo anachoka kunkanso tsidya lija la Yordani, kumalo kumene kunali Yohane analikubatiza poyamba paja; ndipo anakhala komweko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Yesu adabwereranso kutsidya kwa mtsinje wa Yordani, kumene Yohane ankabatizira anthu poyamba paja, ndipo adakhala komweko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Kenaka Yesu anabwereranso kutsidya la mtsinje wa Yorodani kumalo kumene Yohane ankabatiza mʼmasiku akale. Iye anakhala kumeneko Onani mutuwo |