Yohane 10:39 - Buku Lopatulika39 Anafunanso kumgwira Iye; ndipo anapulumuka m'dzanja lao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Anafunanso kumgwira Iye; ndipo anapulumuka m'dzanja lao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Pamenepo anthu aja adafunanso kumgwira, koma Iye adazemba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Iwo anafuna kumugwiranso koma anawapulumuka mʼmanja mwawo. Onani mutuwo |