Yohane 10:4 - Buku Lopatulika4 Pamene adatulutsa zonse nkhosa zimtsata iye; chifukwa zidziwa mau ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pamene adatulutsa zonse nkhosa zimtsata iye; chifukwa zidziwa mau ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Akazitulutsa nkhosa zake zonse, amazitsogolera, izo nkumamtsatira, chifukwa zimadziŵa mau ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Akazitulutsa nkhosa zake zonse, iye amazitsogolera, ndipo nkhosa zakezo zimamutsata chifukwa zimadziwa mawu ake. Onani mutuwo |