Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 10:34 - Buku Lopatulika

34 Yesu anayankha iwo, Kodi sikulembedwa m'chilamulo chanu, Ndinati Ine, Muli milungu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Yesu anayankha iwo, Kodi sikulembedwa m'chilamulo chanu, Ndinati Ine, Muli milungu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Yesu adati, “Kodi m'Malamulo mwanu suja mudalembedwa kuti ‘Mulungu adati, Ndinu milungu?’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Yesu anawayankha kuti, “Kodi sizinalembedwa mʼmalamulo anu kuti, ‘Ine ndanena kuti ndinu milungu?’

Onani mutuwo Koperani




Yohane 10:34
12 Mawu Ofanana  

Ndidzakuyamikani ndi mtima wanga wonse; ndidzaimba zakukulemekezani patsogolo pa milungu.


Mulungu aima mu msonkhano wa Mulungu, aweruza pakati pa milungu.


Usapeputsa oweruza, kapena kutemberera mkulu wa anthu a mtundu wako.


Ndipo iye adzakulankhulira iwe kwa anthu; ndipo kudzatero, kuti iye adzakhala kwa iwe ngati m'kamwa, ndi iwe udzakhala kwa iye ngati Mulungu.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Taona, ndakuika ngati Mulungu kwa Farao; ndi Aroni mkulu wako adzakhala mneneri wako.


Ngati anawatcha milungu iwo amene mau a Mulungu anawadzera (ndipo cholemba sichingathe kuthyoka),


Pamenepo khamulo linayankha Iye, Tidamva ife m'chilamulo kuti Khristu akhala kunthawi yonse; ndipo Inu munena bwanji, kuti Mwana wa Munthu ayenera kukwezedwa? Mwana wa Munthu amene ndani?


Koma chitero, kuti mau olembedwa m'chilamulo chao akwaniridwe, kuti, Anandida Ine kopanda chifukwa.


Inde kudalembedwa m'chilamulo chanu kuti umboni wa anthu awiri uli woona.


Kwalembedwa m'chilamulo, Ndi anthu a malilime ena ndipo ndi milomo ina ndidzalankhula nao anthu awa; ndipo kungakhale kutero sadzamva Ine, anena Ambuye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa