Yohane 10:11 - Buku Lopatulika11 Ine ndine Mbusa Wabwino; mbusa wabwino ataya moyo wake chifukwa cha nkhosa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ine ndine Mbusa Wabwino; mbusa wabwino ataya moyo wake chifukwa cha nkhosa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “Ine ndine mbusa wabwino. Mbusa wabwino amataya moyo wake chifukwa cha nkhosa zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 “Ine ndine Mʼbusa wabwino. Mʼbusa wabwino amataya moyo wake chifukwa cha nkhosa zake. Onani mutuwo |