Yohane 1:49 - Buku Lopatulika49 Natanaele anayankha Iye, Rabi, Inu ndinu Mwana wa Mulungu, ndinu mfumu ya Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Natanaele anayankha Iye, Rabi, Inu ndinu Mwana wa Mulungu, ndinu mfumu ya Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Natanaele adati, “Aphunzitsi, ndinudi Mwana wa Mulungu, ndinu Mfumu ya Israele.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Kenaka Natanieli ananena kuti, “Rabi, Inu ndinu Mwana wa Mulungu; Inu ndinu Mfumu ya Israeli.” Onani mutuwo |