Yohane 1:36 - Buku Lopatulika36 ndipo poyang'ana Yesu alikuyenda, anati, Onani Mwanawankhosa wa Mulungu! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 ndipo poyang'ana Yesu alikuyenda, anati, Onani Mwanawankhosa wa Mulungu! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Pamene adaona Yesu akuyenda, iye adati, “Suuyu Mwanawankhosa wa Mulungu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Iye ataona Yesu akudutsa anati, “Taonani Mwana Wankhosa wa Mulungu!” Onani mutuwo |