Yohane 1:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo Yohane anachita umboni, nati, Ndinaona Mzimu alikutsika kuchokera Kumwamba monga nkhunda; nakhalabe pa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo Yohane anachita umboni, nati, Ndinaona Mzimu alikutsika kuchokera Kumwamba monga nkhunda; nakhalabe pa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Yohane adachitanso umboni, adati, “Ndidaona Mzimu Woyera akutsika kumwamba ngati nkhunda, nakhazikika pa Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Kenaka Yohane anapereka umboni uwu: “Ine ndinaona Mzimu Woyera ngati nkhunda kuchokera kumwamba nakhala pa Iye. Onani mutuwo |