Yeremiya 7:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti mukakonzatu njira zanu ndi machitidwe anu; ndi kuweruzatu milandu ya munthu ndi mnansi wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti mukakonzatu njira zanu ndi machitidwe anu; ndi kuweruzatu milandu ya munthu ndi mnansi wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 “Konzani makhalidwe anu ndi zochita zanu. Muzichitirana zolungama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ngati mutasinthadi makhalidwe anu ndi zochita zanu, ndi kumachitirana zolungama, Onani mutuwo |