Yeremiya 51:3 - Buku Lopatulika3 Wauta asakoke uta wake, asadzikweze m'malaya ake achitsulo; musasiye anyamata ake; muononge ndithu khamu lake lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Wauta asakoke uta wake, asadzikweze m'malaya ake achitsulo; musasiye anyamata ake; muononge ndithu khamu lake lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Okoka uta musaŵalekerere, kapena onyadira chovala chao chankhondo. Anyamata ake musasiyeko ndi mmodzi yemwe. Ankhondo ake onse muŵaononge. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Okoka uta musawalekerere kapena wonyadira chovala chawo chankhondo. Musawasiye anyamata ake kuti akhale ndi moyo; koma muwononge ankhondo ake kotheratu. Onani mutuwo |