Yeremiya 51:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo adzagwa ophedwa m'dziko la Ababiloni, opyozedwa m'miseu yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo adzagwa ophedwa m'dziko la Ababiloni, opyozedwa m'miseu yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Adzavulazidwa ndi kufera m'dziko lonse ndi m'miseu ya mzinda wao womwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Adzavulazidwa ndi kufera mʼdziko la Babuloni lomwelo ndi mʼmisewu yawo yomwe. Onani mutuwo |