Yeremiya 5:8 - Buku Lopatulika8 Anali onga akavalo okhuta mamawa; yense wakumemesera mkazi wa mnansi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Anali onga akavalo okhuta mamawa; yense wakumemesera mkazi wa mnansi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Aliyense ankathamangira mkazi wa mnzake, monga amachitira akavalo onenepa akamamemesa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Monga amachitira akavalo onenepa akamamemesa, aliyense wa iwo ankathamangira mkazi wa mnzake. Onani mutuwo |