Yeremiya 2:4 - Buku Lopatulika4 Tamvani mau a Yehova, iwe nyumba ya Yakobo, ndi inu mabanja onse a nyumba ya Israele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Tamvani mau a Yehova, iwe nyumba ya Yakobo, ndi inu mabanja onse a nyumba ya Israele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Inu zidzukulu za Yakobe, mabanja onse a Israele, mverani mau a Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Imvani mawu a Yehova, inu zidzukulu za Yakobo, inu mafuko onse a Israeli. Onani mutuwo |