Yeremiya 17:2 - Buku Lopatulika2 Pokumbukira ana ao maguwa a nsembe ao ndi zoimiritsa zao kumitengo yaiwisi ya pa zitunda zazitali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pokumbukira ana ao maguwa a nsembe ao ndi zoimiritsa zao kumitengo yaiwisi ya pa zitunda zazitali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Chonsecho ana ao amakumbukira maguwa ao aja ndi zoimiritsa zao zansembe, patsinde pa mtengo wogudira uliwonse, pa mapiri am'dzikomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ngakhale ana awo amakumbukira maguwa awo ndi zoyimiritsa ngati zifanizo za mulungu wawo Asera, pa tsinde la mitengo ya masamba ambiri, pa mapiri aatali mʼdzikomo. Onani mutuwo |