Yakobo 5:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anapempheranso; ndipo m'mwamba munatsika mvula, ndi dziko lidabala zipatso zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anapempheranso; ndipo m'mwamba munatsika mvula, ndi dziko lidabala zipatso zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Atapempheranso, mvula idagwa, nthaka nkuyambanso kumeretsa mbeu zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kenaka anapempheranso, ndipo kumwamba kunagwetsa mvula, ndipo dziko lapansi linatulutsa zomera zake. Onani mutuwo |