Yakobo 4:16 - Buku Lopatulika16 Koma tsopano mudzitamandira m'kudzikuza kwanu; kudzitamandira kulikonse kotero nkoipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma tsopano mudzitamandira m'kudzikuza kwanu; kudzitamandira kulikonse kotero nkoipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma monga zilirimu, mumanyada ndi kudzitama. Kunyada konse kotere nkoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma mmene zililimu mumangodzitama ndi kudzikuza. Kudzitama konse kotereku ndi koyipa. Onani mutuwo |