Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yakobo 4:15 - Buku Lopatulika

15 Mukadanena inu, Akalola Ambuye, ndipo tikakhala ndi moyo, tidzachita kakutikakuti.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Mukadanena inu, Akalola Mulungu, ndipo tikakhala ndi moyo, tidzachita kakutikakuti.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Kwenikweni muyenera kumanena kuti, “Ambuye akalola, tikakhala ndi moyo, tidzachita chakutichakuti.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Koma inuyo muyenera kunena kuti, “Ambuye akalola, tikadzakhala ndi moyo, tidzachita zakutizakuti.”

Onani mutuwo Koperani




Yakobo 4:15
10 Mawu Ofanana  

Muli zolingalira zambiri m'mtima mwa munthu; koma uphungu wa Yehova ndiwo udzaimika.


Ndani anganene, chonena chake ndi kuchitikadi, ngati Ambuye salamulira?


koma anawatsanzika, nati, Akafuna Mulungu, ndidzabwera kwa inu; ndipo anachoka ku Efeso m'ngalawa.


ndi kupempha masiku onse m'mapemphero anga, ngati nkutheka tsopano mwa chifuniro cha Mulungu, ndione ulendo wabwino, wakudza kwa inu.


kuti ndi chimwemwe ndikadze kwa inu mwa chifuniro cha Mulungu, ndi kupumula pamodzi ndi inu.


Pakuti sindifuna kukuonani tsopano popitirira; pakuti ndiyembekeza kukhala ndi inu nthawi, ngati alola Ambuye.


Koma ndidzafika kwa inu msanga, akandilola Ambuye; ndipo ndidzazindikira si mau a iwo odzitukumula, koma mphamvuyi.


Ndipo ichi tidzachita, akatilola Mulungu.


Koma tsopano mudzitamandira m'kudzikuza kwanu; kudzitamandira kulikonse kotero nkoipa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa