Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yakobo 3:11 - Buku Lopatulika

11 Kodi kasupe atulutsira pa uno womwewo madzi okoma ndi owawa?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Kodi kasupe atulutsira pa uno womwewo madzi okoma ndi owawa?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Kodi kasupe amatulutsa madzi omweka ndi oŵaŵa pa dzenje limodzimodzi?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Kodi madzi abwino ndi a mchere angatuluke pa kasupe mmodzi?

Onani mutuwo Koperani




Yakobo 3:11
3 Mawu Ofanana  

Monga kasupe atulutsa madzi ake, chomwecho atulutsa zoipa zake; chiwawa ndi kufunkha zimveka m'kati mwake; pamaso panga masiku onse pali kulira ndi mabala.


Mochokera m'kamwa momwemo mutuluka chiyamiko ndi temberero. Abale anga, izi siziyenera kutero.


Kodi mkuyu ukhoza kubala azitona, abale anga, kapena mpesa kubala nkhuyu? Kotero madzi amchere sangathe kutulutsa okoma.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa