Yakobo 3:10 - Buku Lopatulika10 Mochokera m'kamwa momwemo mutuluka chiyamiko ndi temberero. Abale anga, izi siziyenera kutero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mochokera m'kamwa momwemo mutuluka chiyamiko ndi temberero. Abale anga, izi siziyenera kutero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pakamwa pomwe pamatuluka mayamiko pomweponso pamatuluka matemberero. Abale anga, zoterezi siziyenera kumachitika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mʼkamwa momwemo mutuluka matamando ndi kulalata. Abale anga, zisamatero ayi. Onani mutuwo |