Tito 2:9 - Buku Lopatulika9 Akapolo amvere ambuye ao a iwo okha, nawakondweretse m'zonse; osakana mau ao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Akapolo amvere ambuye ao a iwo okha, nawakondweretse m'zonse; osakana mau ao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Antchito azimvera ambuye ao, aziŵakondweretsa pa zonse. Asamatsutsana nawo Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Phunzitsa akapolo kuti azigonjera ambuye awo mu zinthu zonse ndi kuwakondweretsa. Asamatsutsane nawo Onani mutuwo |