Rute 4:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo woombolayo anati kwa Bowazi, Udzigulire wekha kadzikoko. Navula nsapato yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo woombolayo anati kwa Bowazi, Udzigulire wekha kadzikoko. Navula nsapato yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Choncho pamene wachibale uja adauza Bowazi kuti, “Gulani ndinu mundawo,” adavula nsapato yake napatsa Bowazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Choncho wachibale uja atawuza Bowazi kuti, “Gulani ndinu mundawu.” Iye anavula nsapato yake namupatsa Bowazi. Onani mutuwo |