Rute 4:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anatenga amuna khumi a akulu a mzinda, nati, Mukhale pansi apa. Nakhala pansi iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anatenga amuna khumi a akulu a mudzi, nati, Mukhale pansi apa. Nakhala pansi iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adaitananso atsogoleri khumi amumzindamo naŵauza kuti, “Takhalani pansi apa.” Iwo adakhala pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Bowazi anayitananso akuluakulu khumi a mu mzindamo nati, “Dzakhaleni pansi apa,” ndipo anadzakhala pansi. Onani mutuwo |