Rute 2:5 - Buku Lopatulika5 Nati Bowazi kwa mnyamata woyang'anira ochekawo, Mkazi uyu ngwa yani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Nati Bowazi kwa mnyamata woyang'anira ochekawo, Mkazi uyu ngwa yani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono Bowazi adafunsa kapitao wake amene ankayang'anira anthu okolola aja kuti, “Kodi mai uyu ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Bowazi anafunsa kapitawo wake amene ankayangʼanira okolola aja kuti, “Mayi uyo ndi ndani?” Onani mutuwo |