Rute 1:7 - Buku Lopatulika7 Natuluka iye kumene anakhalako ndi apongozi ake awiri pamodzi naye; nanka ulendo wao kubwerera ku dziko la Yuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Natuluka iye kumene anakhalako ndi apongozi ake awiri pamodzi naye; namka ulendo wao kubwerera ku dziko la Yuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Choncho adanyamuka, pamodzi ndi apongozi akewo, kuchoka kumene ankakhala kuja, nayamba ulendo wobwerera ku dziko la Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Naomi pamodzi ndi apongozi ake awiri aja anachoka kumene ankakhala ndi kuyamba ulendo obwerera kwawo ku Yuda. Onani mutuwo |