Numeri 9:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Mose ananena nao, Baimani; ndimve chouza Yehova za inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Mose ananena nao, Baimani; ndimve chouza Yehova za inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mose adayankha kuti, “Dikirani kuti ndimve zimene Chauta alamule za inu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mose anawayankha kuti, “Dikirani mpaka nditamva zimene Yehova walamula zokhudza Inu.” Onani mutuwo |