Numeri 8:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo atatero alowe Alevi kuchita ntchito ya chihema chokomanako; ndipo uwayeretse, ndi kuwapereka ngati nsembe yoweyula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo atatero alowe Alevi kuchita ntchito ya chihema chokomanako; ndipo uwayeretse, ndi kuwapereka ngati nsembe yoweyula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pambuyo pake Aleviwo adzaloŵa kuti atumikire m'chihema chamsonkhano, utaŵayeretsa ndi kuŵapereka ngati chopereka choweyula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 “Utatha kuyeretsa ndi kupereka Aleviwo monga nsembe yoweyula, apite kukagwira ntchito yawo ku tenti ya msonkhano. Onani mutuwo |