Numeri 8:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo uimike Alevi pamaso pa Aroni, ndi pamaso pa ana ake, ndi kuwapereka ngati nsembe yoweyula kwa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo uimike Alevi pamaso pa Aroni, ndi pamaso pa ana ake, ndi kuwapereka ngati nsembe yoweyula kwa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Uŵauze Aleviwo kuti azitumikira Aroni ndi ana ake aamuna, ndipo uŵapereke kwa Chauta ngati chopereka choweyula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Uyimiritse Aleviwo pamaso pa Aaroni ndi ana ake aamuna ndipo uwapereke ngati nsembe yoweyula kwa Yehova. Onani mutuwo |