Numeri 7:74 - Buku Lopatulika74 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201474 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa74 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzaza ndi lubani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero74 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani; Onani mutuwo |