Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:74 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

74 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

74 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

74 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

74 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzaza ndi lubani,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:74
4 Mawu Ofanana  

Dzina langa lidzalemekezedwa pakati pa mitundu ya anthu, kuchokera kummawa mpaka kumadzulo. Mʼmalo monse adzapereka nsembe zofukiza ndi zopereka zangwiro mʼdzina langa, chifukwa dzina langa lidzakhala lalikulu pakati pa mitundu ya anthu,” akutero Yehova Wamphamvuzonse.


mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani;


Chopereka chakecho chinali mbale imodzi yasiliva yolemera kilogalamu imodzi ndi theka, beseni limodzi lowazira lasiliva lolemera magalamu 800, zonse monga mwa muyeso wa ku malo opatulika; zonse ziwiri zinali zodzaza ndi ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta monga chopereka chachakudya;


mwana wangʼombe wamwamuna mmodzi, nkhosa imodzi yayimuna ndi mwana wankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, za nsembe yopsereza;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa