Numeri 7:72 - Buku Lopatulika72 Tsiku la khumi ndi limodzi kalonga wa ana a Asere, ndiye Pagiyele mwana wa Okarani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201472 Tsiku la khumi ndi limodzi kalonga wa ana a Asere, ndiye Pagiyele mwana wa Okarani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa72 Tsiku la 11 linali la Pagiyele mwana wa Okarani, mtsogoleri wa fuko la Asere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero72 Pa tsiku la khumi ndi chimodzi, Pagieli mwana wa Okirani, mtsogoleri wa fuko la Aseri, anabweretsa chopereka chake. Onani mutuwo |