Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:72 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

72 Pa tsiku la khumi ndi chimodzi, Pagieli mwana wa Okirani, mtsogoleri wa fuko la Aseri, anabweretsa chopereka chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

72 Tsiku la khumi ndi limodzi kalonga wa ana a Asere, ndiye Pagiyele mwana wa Okarani;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

72 Tsiku la khumi ndi limodzi kalonga wa ana a Asere, ndiye Pagiyele mwana wa Okarani;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

72 Tsiku la 11 linali la Pagiyele mwana wa Okarani, mtsogoleri wa fuko la Asere.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:72
4 Mawu Ofanana  

Pagieli mwana wa Okirani, kuchokera ku fuko la Aseri,


Fuko la Aseri lidzamanga pafupi ndi iwowo. Mtsogoleri wa Aaseri ndi Pagieli mwana wa Okirani.


ndi ngʼombe ziwiri zazimuna, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu, ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Ahiyezeri mwana wa Amisadai.


Chopereka chakecho chinali mbale imodzi yasiliva yolemera kilogalamu imodzi ndi theka, beseni limodzi lowazira lasiliva lolemera magalamu 800, zonse monga mwa muyeso wa ku malo opatulika; zonse ziwiri zinali zodzaza ndi ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta monga chopereka chachakudya;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa