Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 7:30 - Buku Lopatulika

30 Tsiku lachinai Elizuri, mwana wa Sedeuri, kalonga wa ana a Rubeni:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Tsiku lachinai Elizuri, mwana wa Sedeuri, kalonga wa ana a Rubeni:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Tsiku lachinai linali la Elizuri mwana wa Sedeuri, mtsogoleri wa Arubeni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Tsiku lachinayi linali la Elizuri mwana wa Sedeuri, mtsogoleri wa fuko la Rubeni, anabweretsa chopereka chake.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:30
4 Mawu Ofanana  

Ndipo maina a amuna amene aime nanu ndi awa: wa Rubeni, Elizuri mwana wa Sedeuri.


Mbendera ya chigono cha Rubeni ikhale kumwera monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Rubeni ndiye Elizuri mwana wa Sedeuri.


ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Eliyabu mwana wa Heloni.


chopereka chake ndicho mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi yasiliva ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika, zonse ziwiri zodzaza ndi ufa wosakaniza ndi mafuta, ukhale nsembe yaufa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa