Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 7:20 - Buku Lopatulika

20 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzadza ndi lubani,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110 yodzaza ndi lubani;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:20
3 Mawu Ofanana  

chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;


anabwera nacho chopereka chake mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi yasiliva ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwiri zodzala ndi ufa wosakaniza ndi mafuta, ukhale nsembe yaufa;


ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa