Numeri 6:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo wansembe azibwera nazo pamaso pa Yehova, nakonze nsembe yake yauchimo, ndi nsembe yake yopsereza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo wansembe azibwera nazo pamaso pa Yehova, nakonze nsembe yake yauchimo, ndi nsembe yake yopsereza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono wansembe abwere nazo zonsezo pamaso pa Chauta. Poyamba apereke nsembe yake yopepesera machimo ndi nsembe yake yopsereza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “Wansembe apereke zimenezi pamaso pa Yehova ndi kuchita nsembe ya uchimo ndi nsembe yopsereza. Onani mutuwo |