Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 5:31 - Buku Lopatulika

31 Mwamunayo ndiye wosachita mphulupulu, koma mkazi uyo asenze mphulupulu yake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Mwamunayo ndiye wosachita mphulupulu, koma mkazi uyo asenze mphulupulu yake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Mwamuna adzakhala wopanda tchimo lililonse, koma mkazi ndiye adzasenza tchimo lake.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Mwamunayo adzakhala wopanda tchimo lililonse, koma mkaziyo adzasenza zotsatira za tchimo lake.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 5:31
8 Mawu Ofanana  

Ndipo adzaonetsa chilungamo chako monga kuunika, ndi kuweruza kwako monga usana.


Taonani, miyoyo yonse ndi yanga, monga moyo wa atate momwemonso moyo wa mwana, ndiyo yanga; moyo wochimwawo ndiwo udzafa.


Munthu akachita chigololo ndi mkazi wa mwini, popeza wachita chigololo ndi mkazi wa mnansi wake, awaphe ndithu, mwamuna ndi mkazi onse awiri.


kapena pamene mtima wansanje umgwira mwamuna, ndipo achitira mkazi wake nsanje; pamenepo aziika mkazi pamaso pa Yehova, ndipo wansembe amchitire chilamulo ichi chonse.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,


Munthu akakhala woyera, wosakhala paulendo, koma akaleka kuchita Paska, amsadze munthuyo kwa anthu a mtundu wake; popeza sanabwere nacho chopereka cha Yehova pa nyengo yake yoikidwa, munthuyu asenze kuchimwa kwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa