Numeri 5:20 - Buku Lopatulika20 Koma iwe, ngati wapatukira mwamuna wako, ngati wadetsedwa, kuti wagona nawe munthu, wosati mwamuna wako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma iwe, ngati wapatukira mwamuna wako, ngati wadetsedwa, kuti wagona nawe munthu, wosati mwamuna wako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Koma ngati udamzemberapo mwamuna wako, ngakhale kuti unali m'manja mwake, nudziipitsa, ndipo ngati udagona ndi mwamuna wina wosakhala mwamuna wako,’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma ngati wayenda njira yoyipa uli pa ukwati ndi mwamuna wako ndi kudzidetsa pogonana ndi mwamuna amene si mwamuna wako,’ Onani mutuwo |