Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 5:12 - Buku Lopatulika

12 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mkazi wamwini akapatukira mwamuna wake, nakamchitira mosakhulupirika,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mkazi wa mwini akapatukira mwamuna wake, nakamchitira mosakhulupirika,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 “Uza Aisraele kuti, mwina mkazi adzazembera mwamuna wake namachita zosakhulupirika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 “Yankhula ndi Aisraeli ndipo uwawuze kuti, ‘Ngati mkazi wa munthu wina ayenda njira yosayenera nakhala wosakhulupirika kwa mwamuna wake,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 5:12
6 Mawu Ofanana  

Usachite chigololo.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,


Ichi ndi chilamulo cha nsanje, pamene mkazi, pokhala naye mwamuna wake, ampatukira nadetsedwa;


Munthu akatenga mkazi akhale wake, kudzali, ngati sapeza ufulu pamaso pake, popeza anapeza mwa iye kanthu kosayenera, amlembere kalata ya chilekanitso, ndi kumpereka uyu m'dzanja lake, ndi kumtulutsa m'nyumba mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa