Numeri 5:10 - Buku Lopatulika10 Zopatulika za munthu aliyense ndi zake: zilizonse munthu aliyense akapatsa wansembe, zisanduka zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Zopatulika za munthu aliyense ndi zake: zilizonse munthu aliyense akapatsa wansembe, zasanduka zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Zopereka zopatulika za munthu aliyense, nzake za iye yemweyo. Koma chilichonse chimene munthu apereka kwa wansembe, nchake cha wansembeyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mphatso zilizonse zopatulika ndi za munthuyo, koma zomwe wapereka kwa wansembe ndi za wansembeyo.’ ” Onani mutuwo |