Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 5:10 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Mphatso zilizonse zopatulika ndi za munthuyo, koma zomwe wapereka kwa wansembe ndi za wansembeyo.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

10 Zopatulika za munthu aliyense ndi zake: zilizonse munthu aliyense akapatsa wansembe, zisanduka zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Zopatulika za munthu aliyense ndi zake: zilizonse munthu aliyense akapatsa wansembe, zasanduka zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Zopereka zopatulika za munthu aliyense, nzake za iye yemweyo. Koma chilichonse chimene munthu apereka kwa wansembe, nchake cha wansembeyo.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 5:10
4 Mawu Ofanana  

Nsembe izi ndi zimene Aisraeli azipereka kwa Aaroni ndi ana ake mwa zonse zimene azipereka nthawi zonse. Mwa zopereka za mtendere zimene ana a Aisraeli adzapereka kwa Yehova, zimenezi zikhale gawo lawo.


Muzidye pa malo wopatulika chifukwa zimenezi ndi gawo lako ndi la ana ako pa zopereka zopsereza kwa Yehova. Izitu ndi zimene Yehova anandilamulira.


Mose anapereka kwa wansembe Eliezara gawo limene linali loyenera kupereka kwa Yehova monga momwe Yehova analamulira Mose.


Kenaka Yehova anawuza Mose kuti,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa