Numeri 4:7 - Buku Lopatulika7 Ndi pa gome la mkate woonekera ayale nsalu yamadzi, naikepo mbale zake, ndi zipande, ndi mitsuko, ndi zikho zakuthira nazo; mkate wa chikhalire uzikhalaponso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndi pa gome la mkate woonekera ayale nsalu yamadzi, naikepo mbale zake, ndi zipande, ndi mitsuko, ndi zikho zakuthira nazo; mkate wa chikhalire uzikhalaponso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ayale nsalu yobiriŵira pa tebulo la buledi wokhala pamenepo nthaŵi zonse, ndi kuikapo mbale zake, zipande zake zotapira lubani, mabeseni ake, ndi zikho za chopereka cha chakumwa. Aikeponso buledi wokhala pamenepo nthaŵi zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 “Pa tebulo pamene pamakhala buledi wa ansembe aziyalapo nsalu ya mtundu wa thambo, ndipo aziyikapo mbale, mabeseni, zipande ndi mitsuko yoperekera nsembe yachakumwa. Aziyikaponso buledi wokhala pamenepo nthawi zonse. Onani mutuwo |