Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 4:48 - Buku Lopatulika

48 owerengedwawo ndiwo zikwi zisanu ndi zitatu kudza mazana asanu mphambu makumi asanu ndi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

48 owerengedwawo ndiwo zikwi zisanu ndi zitatu kudza mazana asanu mphambu makumi asanu ndi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

48 chiŵerengero chao chidakwanira 8,580.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

48 analipo 8,580.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:48
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anawerengedwa Alevi oyambira zaka makumi atatu ndi mphambu, ndipo chiwerengo chao kuwawerenga mmodzimmodzi ndicho amuna zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi zitatu.


Owerengedwa onse a Alevi, adawawerenga Mose ndi Aroni, powauza Yehova, monga mwa mabanja ao, amuna mphambu, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri.


kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa kugwira ntchito ya utumikiwu, ndiyo ntchito ya akatundu m'chihema chokomanako;


Chomwecho omalizira adzakhala oyamba, ndipo oyamba adzakhala omalizira.


Pomwepo Afarisi anamuka, nakhala upo wakumkola Iye m'kulankhula kwake.


Pakuti chipata chili chopapatiza, ndi ichepetsa njirayo yakumuka nayo kumoyo, ndimo akuchipeza chimenecho ali owerengeka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa