Numeri 4:2 - Buku Lopatulika2 Werengani ana a Kohati pakati pa ana a Levi, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Werengani ana a Kohati pakati pa ana a Levi, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mwa ana a Levi muŵerenge ana a Kohati, potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Werengani Akohati omwe ndi gawo limodzi la Alevi monga mwa mafuko awo ndi mabanja awo. Onani mutuwo |