Numeri 36:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo akulu a makolo a mabanja a ana a Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, wa mabanja a ana a Yosefe, anayandikiza, nanena pamaso pa Mose, ndi pamaso pa akalonga, ndiwo akulu a makolo a ana a Israele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo akulu a makolo a mabanja a ana a Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, wa mabanja a ana a Yosefe, anayandikiza, nanena pamaso pa Mose, ndi pamaso pa akalonga, ndiwo akulu a makolo a ana a Israele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Atsogoleri a banja la ana a Giliyadi mwana wa Makiri, mwana wa Manase, limodzi mwa mabanja a adzukulu a Yosefe, adabwera kudzalankhula ndi Mose ndi atsogoleri, akulu a mabanja a makolo a Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Atsogoleri a mabanja a fuko la Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase omwe anali ochokera ku fuko la ana a Yosefe anabwera ndi kuyankhula ndi Mose, atsogoleri ndi akuluakulu a mabanja a Aisraeli. Onani mutuwo |