Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 35:10 - Buku Lopatulika

10 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pakuoloka inu Yordani kulowa m'dziko la Kanani,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pakuoloka inu Yordani kulowa m'dziko la Kanani,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 “Uza Aisraele kuti: Pamene muwoloka mtsinje wa Yordani ndi kuloŵa m'dziko la Kanani,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 “Yankhula ndi Aisraeli kuti, ‘Pamene muwoloka Yorodani kulowa mu Kanaani,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 35:10
9 Mawu Ofanana  

Koma akapanda kumlalira, koma Mulungu akalola akomane ndi mnzake, ndidzakuikirani pothawirapo iye.


Mutakafika m'dziko la Kanani, limene ndikupatsani likhale lanulanu, ndipo ndikaika nthenda yakhate m'nyumba ya dziko lanulanu;


Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mutakalowa m'dziko limene ndikupatsani, dzikoli lizisungira Yehova Sabata.


Uza ana a Israele, nunene nao, Mutalowa m'dziko la Kanani, ndilo dziko logwera inu, likhale cholowa chanu, dziko la Kanani monga mwa malire ake,


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,


pakuti mpaka lero simunafikire mpumulo ndi cholowa, zimene Yehova Mulungu wanu adzakupatsani.


Ndipo Yehova anati kwa Yoswa,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa