Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 34:29 - Buku Lopatulika

29 Iwo ndiwo amene Yehova analamulira agawire ana a Israele cholowa chao m'dziko la Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Iwo ndiwo amene Yehova analamulira agawire ana a Israele cholowa chao m'dziko la Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Ameneŵa ndiwo amene Chauta adalamula kuti agaŵe choloŵa cha Aisraele m'dziko la Kanani.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Awa ndiwo mayina a anthu amene Yehova analamula kuti agawe cholowa cha Aisraeli mʼdziko la Kanaani.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 34:29
4 Mawu Ofanana  

Muwatengenso akalonga, kalonga mmodzi ku fuko limodzi, agawe dziko likhale cholowa chao.


Wa fuko la ana a Nafutali, kalonga Pedahele mwana wa Amihudi.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'zidikha za Mowabu, pa Yordani, ku Yeriko, ndi kuti,


Izi ndizo zolowa anazigawa Eleazara wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a nyumba za atate a mafuko a ana a Israele, zikhale zaozao, ndi kulota maere ku Silo pamaso pa Yehova ku khomo la chihema chokomanako. Momwemo anatha kuligawa dziko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa